Ezekiel 16:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye Chauta akuti, “Uli ndi tsoka, ndithu uli ndi tsoka, chifukwa kuwonjezera pa zoipa zako zonsezo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudachitika utatha zoipa zako zonse, (tsoka iwe, tsoka, ati Ambuye Yehova)
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Tsoka! Tsoka kwa iwe, akutero Ambuye Yehova chifukwa powonjezera pa zoyipa zako zonse,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudacitika utatha zoipa zako zonse, (tsoka iwe, tsoka, ati Ambuye Yehova)