Ezekiel 16:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
udadzimangira nsanja pamodzi ndi guwa lake pa bwalo lililonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
unadzimangira nyumba yachimphuli, unadzimangiranso chiunda m'makwalala ali onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wadzimangira wekha nsanja ndi guwa pa mabwalo onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
unadzimangira nyumba yacimphuli, unadzimangiranso ciunda m'makwalala ali onse.