Ezekiel 16:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udachita zigololo ndi Aejipito adama oyandikana nawe, ndipo udandikwiyitsa chifukwa udachulukitsa zigololo zako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wachitanso chigololo ndi Ejipito oyandikizana nawe, akulu thupi, ndi kuchulukitsa chigololo chako kuutsa mkwiyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Umachita chigololo ndi Aigupto, anthu adama oyandikana nawe. Choncho unandikwiyitsa chifukwa unachulukitsa za dama zako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wacitanso cigololo ndi Aaigupto oyandikizana nawe, akulu thupi, ndi kucurukitsa cigololo cako kuutsa mkwiyo wanga.