Ezekiel 16:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha zilakolako zako udachitanso chigololo ndi Aasiriya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Unachitanso chigololo ndi Aasiriya, pakuti unakhala wosakoledwa, inde unachita chigololo nao, koma sunakoledwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha chilakolako chako unachitanso zadama ndi Aasiriya. Ngakhale unachita nawo chigololo koma sunakhutitsidwebe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Unacitanso cigololo ndi Aasuri, pakuti unakhala wosakoledwa, inde unacita cigololo nao, koma sunakoledwa.