Ezekiel 16:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkazi wadama iwe, unkakonda amuna achilendo kupambana mwamuna wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiwe mkazi wokwatibwa wochita chigololo, wolandira alendo m'malo mwa mwamuna wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Iwe mkazi wachigololo! Umakonda amuna achilendo kupambana mwamuna wakowako!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiwe mkazi wokwatibwa wocita cigololo, wolandira alendo m'malo mwa mwamuna wace.