Ezekiel 16:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakulanga monga amalangira akazi achigololo ndiponso opha anthu. Chifukwa cha nsanje yanga ndidzakhetsa magazi ako mokwiya kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzaweruza mlandu wako, monga aweruza akazi achigololo ndi okhetsa mwazi; ndipo ndidzakutengera mwazi wa ukali ndi wa nsanje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzakulanga monga mmene amalangira akazi amene amachita chigololo ndiponso opha anthu. Chifukwa cha ukali wanga ndi nsanje yanga, ndidzakhetsa magazi ako mokwiya kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzaweruza mlandu wako, monga aweruza akazi acigololo ndi okhetsa mwazi; ndipo ndidzakutengera mwazi wa ukali ndi wa nsanje.