Ezekiel 16:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe Yerusalemu, akuluakulu adzakuphera mwambi uwu wakuti, ‘Mwana watengera cha make.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, aliyense wonena miyambi adzakunenera mwambi uwu, wakuti, Monga make momwemo mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Taona, onse onena miyambi adzakuphera mwambi wakuti, ‘Make mbuu, mwana mbuu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, ali yense wonena miyambi adzakunenera mwambi uwu, wakuti, Monga mace momwemo mwana wace.