Ezekiel 16:50 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankadzitukumula kwambiri namachita zonyansa zambiri pamaso panga. Nchifukwa chake ndidaŵachotsa monga m'mene waoneramu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadzikuza, nachita chonyansa pamaso panga; chifukwa chake ndinawachotsa pakuchiona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anali odzitukumula ndipo ankachita zonyansa pamaso panga. Nʼchifukwa chake ndinawachotsa monga mmene waoneramu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadzikuza, nacita conyansa pamaso panga; cifukwa cace ndinawacotsa pakuciona.