Ezekiel 16:54 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho uchite manyazi ndi kunyozedwa, chifukwa udaonetsa abale akoŵa ngati angwiro.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti usenze manyazi ako, ndi kuti uchite manyazi chifukwa cha zonse unazichita pakuwatonthoza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzatero kuti uchite manyazi ndi kunyozeka chifukwa cha zonse zimene unachita powatonthoza anthuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti usenze manyazi ako, ndi kuti ucite manyazi cifukwa ca zonse unazicita pakuwatonthoza.