Ezekiel 16:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo ukule ngati mbeu ya m'munda.” Udakuladi, ndipo udatalika nkutha msinkhu. Maŵere adayamba kumera, tsitsi lako lidayamba kutalika. Komabe unali wamaliseche ndi wausiŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinakuchulukitsa ngati mphundu za kumunda; ndipo unathululuka ndi kukula kufikira wakongola nkhope, mawere ako anamera, ndi tsitsi lako linamera; koma unali wamaliseche ndi wausiwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi kuti ukule ngati mbewu ya mʼmunda. Iwe unakula ndipo unatalika ndi kutha msinkhu. Mawere ako anayamba kumera ndi tsitsi lakonso linayamba kutalika. Komabe unali wamaliseche ndi wausiwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinakucurukitsa ngati mphundu za kumunda; ndipo unathululuka ndi kukula kufikira wakongola nkhope, maere ako anamera, ndi tsitsi lako linamera; koma unali wamarisece ndi wausiwa.