Ezekiel 16:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“ ‘Tsono ndidakusambitsa m'madzi ndi kukutsuka magazi ako, ndipo ndidakudzoza mafuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinakusambitsa ndi madzi, inde ndinakutsuka kukuchotsera mwazi wako, ndi kukudzoza mafuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ine ndinakusambitsa mʼmadzi kutsuka magazi ako ndikukudzoza mafuta.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinakusambitsa ndi madzi, inde ndinakutsuka kukucotsera mwazi wako, ndi kukudzoza mafuta.