Ezekiel 17:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Idatenga mwana wina wa mfumu nkuchita naye chipangano, ndipo idamlumbiritsa kuti akhale womvera. Idachotsa akulu onse am'dzikomo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nitenga wa mbumba yachifumu, nichita naye pangano, nimlumbiritsa, nichotsa amphamvu a m'dziko;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anatenga mmodzi wa banja laufumu ndi kuchita naye mgwirizano, ndipo anamulumbiritsa kuti akhale womvera. Inatenganso akulu onse a mʼdzikomo
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nitenga wa mbumba yacifumu, nicita naye pangano, nimlumbiritsa, nicotsa amphamvu a m'dziko;