Ezekiel 17:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, uŵaphere mwambi Aisraele ndi kuŵauza fanizo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, ipha mwambi, nunene fanizo kwa nyumba ya Israele,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, aphere mwambi anthu a Israeli ndi kuwawuza fanizo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobadwa ndi munthu iwe, ipha mwambi, nunene fanizo kwa nyumba ya Israyeli,