Ezekiel 17:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nkubudula nsonga yeniyeni ya nthambiyo. Chidapita nayo ku dziko lamalonda, nkukaiika mu mzinda wa anthu amalonda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chinabudula nsonga yosomphoka ya nthambi zake zanthete, ndi kumuka nayo kudziko la malonda, chinaiika m'mudzi wa amalonda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chinabudula msonga yeniyeni ya nthambiyo nʼkupita nayo ku dziko lamalonda ndipo anakayika mu mzinda wa anthu amalonda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cinabudula nsonga yosomphoka ya nthambi zace zanthete, ndi kumuka nayo ku dziko la malonda, cinaiika m'mudzi wa amalonda.