Ezekiel 17:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka chidatenga mbeu ya m'dzikomo nkukaibzala pa malo achonde, pamene panali madzi ambiri pafupi. Chidaibzala monga momwe amabzalira mtengo wa msondodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinatengakonso mbeu ya m'dziko, ndi kuibzala m'nthaka yokoma, chinaiika panali madzi ambiri, chinaioka ngati mtengo wamsondodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Kenaka chinatenga mbewu ina ya mʼdziko ndi kukayidzala ku malo a chonde kumene kunali madzi ambiri. Anayidzala ngati mmene amadzalira mtengo wa msondozi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinatengakonso mbeu ya m'dziko, ndi kuibzala m'nthaka yokoma, cinaiika panali madzi ambiri, cinaioka ngati mtengo wamsondodzi.