Ezekiel 17:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mtengowo adaauwoka kale m'nthaka yachonde m'mene munali madzi ambiri, kuti uphuke nthambi ndi kubereka mphesa, ndi kukhala wokongola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Unaokedwa mu nthaka yabwino kuli madzi ambiri, kuti uphuke nthambi, nubale zipatso, nukhale mpesa wabwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mtengowo unadzalidwa kale pa nthaka yabwino mʼmbali mwa madzi kuti ukhale ndi nthambi zambiri, ubereke zipatso ndi kukhala wokongola.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Unaokedwa mu nthaka yabwino kuli madzi ambiri, kuti uphuke nthambi, nubale zipatso, nukhale mpesa wabwino.