Ezekiel 19:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“ ‘Mai wako anali ngati mpesa m'munda wa mphesa wobzalidwa m'mbali mwa madzi. Udabereka bwino ndipo unali ndi nthambi zambiri, chifukwa panali madzi ambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mai wako ananga mpesa wookedwa kumadzi; muja anakhala mumtendere unabala zipatso, wodzala ndi nthambi, chifukwa cha madzi ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Amayi ako anali ngati mpesa mʼmunda wamphesa wodzalidwa mʼmbali mwa madzi. Unabereka bwino ndipo unali ndi nthambi zambiri chifukwa cha kuchuluka kwa madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mai wako ananga mpesa wookedwa kumadzi; muja anakhala mumtendere unabala zipatso, wodzala ndi nthambi, cifukwa ca madzi ambiri.