Ezekiel 19:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adalera mmodzi mwa ana ake, ndipo mwanayo adasanduka mkango. Udaphunzira kugwira nyama, nuyamba kudya anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo unalera mmodzi wa ana ake, iye nasanduka msona, unaphunzira kugwira nyama, unalusira anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Unalera mmodzi mwa ana ake, ndipo mwanayo anasanduka mkango wamphamvu. Unaphunzira kugwira nyama, ndipo unayamba kudya anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo unalera mmodzi wa ana ace, iye nasanduka msona, unaphunzira kugwira nyama, unalusira anthu.