Ezekiel 19:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mai uja ataona kuti mwana ankamukhulupirirayu wagwidwa, adakuzanso wina mwa ana ake, namsandutsa mkango wamphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuona tsono waukaziwo, kuti unalindirira, ndi kuti chiyembekezo chake chidatha, unatenga wina wa ana ake, numsandutsa msona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Amayi aja ataona kuti mwana ankamukhulupirira uja wagwidwa ndi kuti chiyembekezo chake chapita padera, amayiwo anatenganso mwana wina namusandutsa mkango wamphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuona tsono waukaziwo, kuti unalindirira, ndi kuti ciyembekezo cace cidatha, unatenga wina wa ana ace, numsandutsa msona.