Ezekiel 19:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mitundu ya anthu, makamaka a m'maiko ozungulira, adabwera kudzalimbana nawo. Adautchera ukonde, ndipo udagweradi m'mbuna yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mitundu ya anthu inadzipereka kuukola kuchokera kumaiko a kumbali zonse, niuphimba ndi ukonde wao, nugwidwa uwu m'mbuna mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mitundu ya anthu, makamaka ochokera madera ozungulira, inabwera kudzalimbana nawo. Anawutchera ukonde wawo, ndipo tsiku lina unagwera mʼmbuna mwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mitundu ya anthu inadzipereka kuukola kucokera ku maiko a ku mbali zonse, niuphimba ndi ukonde wao, nugwidwa uwu m'mbuna mwao.