Ezekiel 2:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mauwo adati, “Munthu iwe, imirira ndilankhule nawe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, khala chilili, ndipo ndidzanena nawe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anandiwuza kuti, “Iwe mwana wa munthu, imirira kuti ndiyankhule nawe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, khala ciriri, ndipo ndidzanena nawe.