Ezekiel 2:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye popeza kuti iwowo ngaupandu, kaya akamvera kaya akakana, (pakuti ndi anthu opanduka) koma adzadziŵa ndithu kuti mneneri wafikadi pakati pao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwowa, ngakhale akamva kapena akaleka kumva, (pakuti ndiwo nyumba yopanduka,) koma adzadziwa kuti panali mneneri pakati pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kaya akamva kaya sakamvera, pakuti iwo ndi anthu opanduka, komabe adzadziwa kuti mneneri ali pakati pawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwowa, ngakhale akamva kapena akaleka kumva, (pakuti ndiwo nyumba yopanduka,) koma adzadziwa kuti panali mneneri pakati pao.