Ezekiel 20:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaŵapatsa malangizo anga kumeneko, ndi kuŵaphunzitsa malamulo anga, amene amakhalitsa moyo anthu oŵamvera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinawapatsanso malemba anga, ndi kuwadziwitsa maweruzo anga, ndiwo munthu akawachita adzakhala nao ndi moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinawapatsa malangizo anga ndi kuwadziwitsa malamulo anga amene munthu aliyense akawamvera adzakhala ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinawapatsanso malemba anga, ndi kuwadziwitsa maweruzo anga, ndiwo munthu akawacita adzakhala nao ndi moyo.