Ezekiel 20:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuwonjezera pamenepo, ndidalumbira kwa iwo m'chipululu nditakweza dzanja, kuti sindidzaŵaloŵetsa m'dziko limene ndinali nditaŵapatsa, dziko lamwanaalirenji, lokoma kwambiri kupambana maiko ena onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinawakwezeranso dzanja langa m'chipululu, kusawalowetsa m'dzikolo ndidawapatsa, moyenda mkaka ndi uchi, ndilo lokometsetsa mwa maiko onse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinalumbiranso kwa iwo mʼchipululu muja, nditakweza dzanja, kuti sindidzawalowetsanso mʼdziko limene ndinawapatsa, dziko la mwana alirenji, lokoma kwambiri kuposa mayiko ena onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinawakwezeranso dzanja langa m'cipululu, kusawalowetsa m'dzikolo ndidawapatsa, moyenda mkaka ndi uci, ndilo lokometsetsa mwa maiko onse;