Ezekiel 20:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma sindidachite zimenezo, kuti choncho dzina langa lilemekezeke, lisanyozeke pakati pa anthu a mitundu ina amene adandiwona ndikutulutsa Aisraelewo ku Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndinabweza dzanja langa ndi kuchichita, chifukwa cha dzina langa; kuti lisaipsidwe pamaso pa amitundu, amene ndinawatulutsa pamaso pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma sindinatero chifukwa cha dzina langa kuti lisayipitsidwe pakati pa anthu a mitundu ina amene anandiona ndikutulutsa Aisraeliwo mu Iguptomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndinabweza dzanja langa ndi kucicita, cifukwa ca dzina langa; kuti lisaipsidwe pamaso pa amitundu, amene ndinawaturutsa pamaso pao. Ndinawakwezeranso dzanja langa m'cipululu,