Ezekiel 20:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inuyo mukufuna kukhala ngati anthu a mitundu ina, ngati anthu a m'maiko ena amene amapembedza mitengo ndi miyala. Koma zimenezo sizidzachitika konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi ichi chimauka mumtima mwanu sichidzachitika, umo mukuti, Tidzakhala ngati amitundu, ngati mabanja a m'maiko, kutumikira mtengo ndi mwala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Inu munanena kuti, ‘Tikufuna tikhale ngati anthu a mitundu ina, ngati anthu adziko lapansi, amene amapembedza mtengo ndi mwala.’ Koma zimene mukuganizazo sizidzachitika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi ici cimauka mumtima mwanu sicidzacitika, umo mukuti, Tidzakhala ngati amitundu, ngati mabanja a m'maiko, kutumikira mtengo ndi mwala.