Ezekiel 20:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi dzanja langa lamphamvu ndi mkono wanga wosamula kuwonetsa mkwiyo, ndidzakuchotsani pakati pa mitundu ina ya anthu ndi kukusonkhanitsani kuchokera kumaiko kumene mudabalalikirako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzakutulutsani mwa mitundu ya anthu, ndi kukusonkhanitsani m'maiko munabalalikamo ndi dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka, ndi ukali wotsanulidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakuchotsani pakati pa anthu a mitundu ina ndikukusonkhanitsani kuchokera ku mayiko kumene munamwazikirako, ndi dzanja langa lamphamvu ndi lotambasuka ndili wokwiya kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakuturutsani mwa mitundu ya anthu, ndi kukusonkhanitsani m'maiko munabalalikamo ndi dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka, ndi ukali wotsanulidwa.