Ezekiel 20:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndidzakuŵerengani ndi ndodo ya mbusa, ndi kukuloŵetsani m'chigwirizano cha chipangano changa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzakupititsani pansi pa ndodo ya mbusa ndi kukulowetsani m'chimango cha chipangano;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakuwerengani ndi ndodo ya mʼbusa, kukulowetsani mʼchimango cha pangano langa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakupititsani pansi pa ndodo ya mbusa ndi kukulowetsani m'cimango ca cipangano;