Ezekiel 20:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, kodi ukuvomera kudzaŵaweruza? Kodi udzagamula mlandu wao? Tsonotu uŵafotokozere zonyansa zonse zimene adachita makolo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzawaweruza kodi, wobadwa ndi munthu iwe? Udzawaweruza? Uwadziwitse zonyansa za makolo ao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi uwaweruza? Iwe mwana wa munthu, kodi ugamula mlandu wawo? Uwadziwitse tsono zonyansa zimene anachita makolo awo, uwawuze kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzawaweruza kodi, wobadwa ndi munthu iwe? udzawaweruza? uwadziwitse zonyansa za makolo ao,