Ezekiel 20:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mudzadziŵa kuti Ine ndine Chauta, ndikadzakubwezerani kwanu ku dziko la Israele, dziko limene ndidachita kulumbira kuti ndidzapatsa makolo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakukulowetsani Ine m'dziko la Israele, m'dzikoli ndinalikwezera dzanja langa kulipereka kwa makolo anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mudzadziwa kuti ndine Yehova ndikadzabwera nanu ku dziko la Israeli, dziko limene ndinalumbira kuti ndidzapereka kwa makolo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakukulowetsani Ine m'dzil ko la Israyeli, m'dzikoli ndinalikwezera dzanja langa kulipereka kwa makolo anu.