Ezekiel 20:48 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse adzadziŵa kuti Ine Chauta ndine amene ndauyatsa motowo, ndipo sudzazimidwadi.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi anthu onse adzaona kuti Ine Yehova ndinauyatsa, sudzazimika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense adzadziwa kuti Ine Yehova ndi amene ndayatsa motowo, ndipo sudzazimitsidwa.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi anthu onse adzaona kuti Ine Yehova ndinauyatsa, sudzazimika.