Ezekiel 20:49 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndidati, “A! Inu Ambuye Chauta, anthu akundinena, akuti, ‘Suja amangonena nthano chabe ameneyu!’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ndinati, Ha, Ambuye Yehova! Anandinena, Wonena mafanizo uyu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ine ndinati, “Aa, Ambuye Yehova! Anthu akungondinena kuti, ‘Kodi suja amangonena nthano chabe ameneyu!’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndinati, Ha, Ambuye Yehova! anandinena, Wonena mafanizo uyu.