Ezekiel 21:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alinola kuti likaphe, alipukuta kuti ling'anipe ngati mphezi. Kodi tingakondwere bwanji, pamene anthu anga anyoza ndodo yanga yolangira?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
lanoledwa kuti liphetu, lituulidwa kuti linge mphezi; tisekererepo kodi? Ndilo ndodo yachifumu ya mwana wanga, yopeputsa mtengo uliwonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lanoledwa kuti likaphe, lapukutidwa kuti lingʼanime ngati mphenzi! “ ‘Kodi tingakondwere bwanji? Wanyoza ndodo, mwana wanga ndi chilichonse cha mtengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
lanoledwa kuti liphetu, lituulidwa kuti linge mphezi; tisekererepo kodi? ndilo ndodo yacifumu ya mwana wanga, yopeputsa mtengo uli wonse.