Ezekiel 21:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lupanga laperekedwa kuti alipukute ndipo kuti alinyamule. Lupanga limeneli lanoledwa ndi kupukutidwa, kuti alipereke m'manja mwa munthu amene amapha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analipereka alituule, kuti achite nalo lupangali analinola, inde analituula kulipereka m'dzanja la wakupha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Lupanga laperekedwa kuti lipukutidwe, ndi kuti linyamulidwe, lanoledwa ndi kupukutidwa, kuti liperekedwe mʼmanja mwa munthu amene amapha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analipereka alituule, kuti acite nalo lupangali analinola, inde analituula kulipereka m'dzanja la wakupha.