Ezekiel 22:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nchifukwa chake Ine ndichita kuti m'manja bu nkudabwa kwambiri chifukwa cha phindu lako lopeza monyenga, ndiponso chifukwa cha kuphana kumene kumachitika m'kati mwa malinga ako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, ndaomba manja pa phindu lako lonyenga waliona, ndi pa mwazi wokhala pakati pako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Koma Ine ndachita kuwomba mʼmanja kuti phuu nʼkudabwa chifukwa cha phindu lachinyengo limene mwapeza ndiponso chifukwa cha kuphana kumene kumachitika pakati panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, ndaomba manja pa phindu lako lonyenga waliona, ndi pa mwazi wokhala pakati pako.