Ezekiel 22:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mtima wako udzakhala wolimbabe ndiponso manja ako adzakhalabe amphamvu, ndikadzatsiriza kukulanga? Ine Chauta ndatero, ndipo ndidzazichitadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wako udzaimika kodi, manja ako adzalimbikira masikuwo ndidzachita nawe? Ine Yehova ndanena, ndidzachichita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mtima wako udzakhala wolimbabe kapena manja ako adzakhalabe amphamvu ndikadzatsiriza kukulanga iwe? Ine Yehova ndayankhula, ndipo ndidzazichitadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wako udzaimika kodi, manja ako adzalimbikira masikuwo ndidzacita nawe? Ine Yehova ndanena, ndidzacicita.