Ezekiel 22:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzabalalitsa anthu ako pakati pa mitundu ina ya anthu ndi kuŵamwazira ku maiko akutali. Ndimo m'mene ndidzakuchotsere kuipa kwako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzakumwaza mwa amitundu, ndi kukubalalitsa m'maiko, ndi kukuthera zodetsa zako zikuchokere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina ndi kukumwazirani ku mayiko onse. Umu ndi mmene ndidzachotsere zoyipa zako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakumwaza mwa amitundu, ndi kukubalalitsa m'maiko, ndi kukuthera zodetsa zako zikucokere.