Ezekiel 22:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, Aisraele onse asanduka achabechabe m'maso mwanga. Akulingana ndi mkuŵa, chitini, chitsulo ndi mtovu, zimene zatsala m'ng'anjo atayeretsa siliva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, nyumba ya Israele yandikhalira mphala; onsewo ndiwo mkuwa, ndi seta, ndi chitsulo, ndi ntovu, m'kati mwa ng'anjo; ndiwo mphala zasiliva.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, Aisraeli asanduka chinthu cha chabechabe kwa Ine. Onse ali ngati mkuwa, chitini, chitsulo ndi mtovu zotsala mʼngʼanjo atayeretsa siliva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobadwa ndi munthu iwe, nyumba ya Israyeli yandikhalira mphala; onsewo ndiwo mkuwa, ndi seta, ndi citsulo, ndi ntobvu, m'kati mwa ng'anjo; ndiwo mphala zasiliva.