Ezekiel 22:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, kodi ukufuna kudzaweruza Yerusalemu? Kudzaweruza mzinda wodzaza ndi anthu opha anzaoŵa? Tsono uudzudzule chifukwa cha machitidwe ake onse onyansa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, udzaweruza, udzauweruza mudziwo wa mwazi kodi? Uudziwitse tsono zonyansa zake zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, kodi udzaweruza mzinda uwo wa anthu akupha anzawo? Tsono uwudzudzule chifukwa cha machitidwe ake onse onyansa
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, udzaweruza, udzauweruza mudziwo wa mwazi kodi? uudziwitse tsono zonyansa zace zonse.