Ezekiel 22:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atsogoleri ake ali ngati mimbulu yokadzula nyama. Amakhetsa magazi ndi kuwononga moyo wa anthu, kuti apate phindu loipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akalonga ake m'kati mwake akunga mimbulu yakumwetula nyama, kukhetsa mwazi, kuononga miyoyo, kuti aone phindu lonyenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atsogoleri ake ali ngati mimbulu yokhadzula nyama; amakhetsa magazi ndi kupha anthu kuti apeze phindu loyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akalonga ace m'kati mwace akunga afisi akumwetula nyama, kukhetsa mwazi, kuononga miyoyo, kuti aone phindu lonyenga.