Ezekiel 22:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maiko apafupi ndi akutali omwe adzakunyodola, iwe wa mbiri yoipawe ndi wokonda zandeu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Okhala pafupi ndi okhala patali adzakuseka pwepwete, wodetsedwa dzina iwe, wodzala ndi kusokosera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayiko amene ali pafupi ndi mayiko omwe ali kutali adzakunyoza, iwe mzinda wa mbiri yoyipa, wodzaza ndi chiwawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Okhala pafupi ndi okhala patali adzakuseka pwepwete, wodetsedwa dzina iwe, wodzala ndi kusokosera.