Ezekiel 22:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Taona m'mene akuluakulu onse okhala mwa iwe amaphera anthu anzao, aliyense potsata mphamvu zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona akalonga a Israele, yense monga mwa mphamvu yake, akhala mwa iwe, kuti akhetse mwazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Taona momwe aliyense wa atsogoleri a Israeli amagwiritsira mphamvu zake kupha anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona akalonga a Israyeli, yense monga mwa mphamvu yace, akhala mwa iwe, kuti akhetse mwazi.