Ezekiel 22:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wanyoza zinthu zanga zopatulika, ndipo waipitsa masiku anga a Sabata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wanyoza zopatulika zanga, waipsa masabata anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wanyoza zinthu zanga zopatulika ndi kuyipitsa Masabata anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wanyoza zopatulika zanga, waipsa masabata anga.