Ezekiel 23:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono Oholiba mng'ono wake uja adatengerako, ndipo adachita zadama kupambana mkulu wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene mng'ono wake Oholiba anachiona, anavunda ndi kuumirira kwake koposa iyeyo; ndi zigololo zake zidaposa zigololo za mkulu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mphwake Oholiba anaona zimenezi natengerako. Koma iye anachita zachiwerewere kuposa mkulu wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene mng'ono wace Oholiba anaciona, anabvunda ndi kuumirira kwace koposa iyeyo; ndi zigololo zace zidaposa zigololo za mkuru wace.