Ezekiel 23:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma Oholiba uja adachita chigololo kopitirira mkulu wake. Adaona zithunzi za amuna pa makoma, zithunzi za Ababiloni zolembedwa ndi utoto wofiira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaonjeza zigololo zake, naona amuna olembedwa pakhoma, zithunzithunzi za Ababiloni olembedwa ndi kundwe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma Oholiba uja anachita chigololo kopitirira mkulu wake. Iye anaona zithunzi za amuna pa khoma, zithunzi za Ababuloni zolembedwa ndi inki yofiira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaonjeza zigololo zace, naona amuna olembedwa pakhoma, zithunzithunzi za Akasidi olembedwa ndi kundwe;