Ezekiel 23:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, panali akazi aŵiri, ana a mimba imodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, panali akazi awiri, mai wao ndi mmodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, panali atsikana awiri ana a mayi mmodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobadwa ndi munthu iwe, panali akazi awiri, mai wao ndi mmodzi;