Ezekiel 23:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankalakalaka abwenzi ake amene ziwalo zao zinali zazikulu ngati za bulu, amene kutentha kwao kunali ngati kwa akavalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaumirira amuna ao amene nyama yao ikunga ya abulu, ndi kutentha kwao ngati kutentha kwa akavalo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumeneko iye ankalakalaka zibwenzi zake, amene ziwalo zawo zinali ngati za abulu ndipo kutentha kwawo kunali ngati kwa akavalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaumirira amuna ao amene nyama yao ikunga ya aburu, ndi kutentha kwao ngati kutentha kwa akavalo.