Ezekiel 23:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nchifukwa chake Ine Ambuye Chauta ndikuti, Iwe Oholiba, ndidzakuutsira zibwenzi zako zimene udanyansidwa nazozo kuti zilimbane nawe. Ndidzaziitana kuti zibwere kwa iwe kuchokera ku mbali zonse
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake, Oholiba, atero Ambuye Yehova, Taona ndidzakuutsira mabwenzi ako amene moyo wako wakufidwa nao, ndi kukufikitsira iwowa pozungulira ponse atsutsane nawe,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsono iwe Oholiba, Ine Ambuye Yehova ndikuti: Ndidzakudzutsira zibwenzi zako zimene unkanyansidwa nazo zija kuti zilimbane nawe. Ndidzaziyitana kuti zibwere kuchokera mbali zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace, Oholiba, atero Ambuye Yehova, Taona ndidzakuutsira mabwenzi ako amene moyo wako wakufidwa nao, ndi kukufikitsira iwowa pozungulira ponse atsutsane nawe,