Ezekiel 23:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankachita zadama ku Ejipito. Zadamazo ankachita akali atsikana. Kumeneko anthu ankangoŵasisita pa chifuwa ndi kumaŵagwira maŵere ao osagwa aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anachita chigololo iwo m'Ejipito, anachita chigololo m'ubwana wao; pomwepo anthu anasindikiza mawere ao, pomweponso anakhudza nsonga za mawere za unamwali wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo ankachita za chiwerewere ku Igupto. Za chiwerewerezo anayamba ali achichepere. Kumeneko anthu ankangowasisita pa chifuwa ndi kuwagwiragwira mawere awo aja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anacita cigololo iwo m'Aigupto, anacita cigololo m'ubwana wao; pomwepo anthu anasindikiza maere ao, pomweponso anakhudza nsonga za maere za unamwali wao.