Ezekiel 23:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndizo zakubweretsera zimenezi, chifukwa choti wachita zonyansa ndi mitundu ya anthu achilendo, ndi kudziipitsa ndi mafano ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Izi adzakuchitira chifukwa watsata amitundu, ndi kuchita nao chigololo, popezanso wadetsedwa ndi mafano ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zabweretsa izi pa iwe chifukwa unachita zonyansa ndi anthu a mitundu ndi kudziyipitsa ndi mafano awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Izi adzakucitira cifukwa watsata amitundu, ndi kucita nao cigololo, popezanso wadetsedwa ndi mafano ao.